Alandidwa Katundu Chifukwa Chokanika Kubwedza Ndalama Ya Bank Nkhonde

Mzimayi wina ku lilongwe, walandidwa katundu wake wa mnyumba chifukwa chokanika kubweza ndalama ya bank nkhonde (VIllage Bank).
Mauthenga akuti mmayiyu wakanika kubweza ndalama yokwana 1.8 million kwacha.


Comments

Popular posts from this blog

Airtel money reduces cash out fees to Malawi customers