Mgwilizano wa Tonse Alliance watsutsa mphekesera zomwe zikumveka pa Social Media zonena kuti kuli mpungwepungwe ku Tonse Alliance.
Tonse Alliance yanena kuti pulezidenti Dr Lazarus Chakwera pamodzi ndi wachiwiri wake Dr Saulos Chilima akugwira ntchito limodzi bwino bwino yolimbana ndi kuthetsa mavuto omwe alipo m'dziko muno omwe anayambitsidwa ndi utsogoleri wa pulezidenti yemwe anachoka pasanabwere a Chakwera.

Comments
Post a Comment