ADZIPHA KU NYUMBA YA CHIBWEZI CHAKE



Uyu ndi Shakirah Wenga ndipo amakhala ku Karonga.Tsikanayu adachoka ku Mudzi kwawo kupita ku Kasungu kwa Chibwezi chake chomwe ndi Msilikali kuti akacheze.
Image may contain: 1 person, closeup

Ndipo adafikadi dzuro pa Nyumbapo ndipo adacheza mpaka mamunayo adamusazika Shakirah kuti akupita ku Ntchito usiku monga mwa Ntchito za Usilikali.

Koma kucha kwa lero mamuna atabwelera pa Nyumba kuchoka ku Ntchito kuja adapeza Shakirah atazimangilira.Koma chomwe chapangitsa kuti mkaziyu adziphe sichikudziwika ndipo tikadafufuzabe kuti tidziwe kuti nchiyani.

Comments

Popular posts from this blog

Airtel money reduces cash out fees to Malawi customers